Chichewa Paper 2






chonde onetsesani kuti mwalemba whatsApp number yolondolola chifukwa zotsatila zizatumidzidwa kwa inu kuzera pa whatsaApp pasadathe maola 24

MALANGIZO

Yakhani futso polemba yakho lanu kati mwaka bokosi kosonyezedwa.
Yesetsani kulemba pepalali kwa 1hr kapena isakwane.
Tumizani zomwe mwayakha popanga click batani la submint .

Malamulo a chiyankhulo

1.a.Kodi mayina awa adachokera ku chiyankhulo chanji?(malikisi 4)

1.b kodi afotokozi ali m`munsiwa adapangidwa bwanji? (maliki 6)

2.a.Pangani ziganizo ndi nthawi za aneni zotsatirazi: (malikisi 6)

2.b.Tchulani mitundu ya agwirizanitsi omwe ali ndi mzere kunsi kwake mu ziganizo zotsatirazi (malikisi 4)

3.a. Lembani ziganizo zosonyeza ntchito za ‘ti’ zotsatirazi ndipo mutseke mzere kunsi kwake (malikisi 6)

Tchulani ntchito za akapandamneni omwe atsekedwa mzere kunsi kwawo mziganizo zotsatirazi. (malikisi 4)

4.Phwanyani chiganizo chotsatirachi pounika mawu aliwonse pawokhapawokha